Luka 12:13 - Buku Lopatulika13 Ndipo munthu wa m'khamulo anati kwa Iye, Mphunzitsi, uzani mbale wanga agawane ndi ine chuma chamasiye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Ndipo munthu wa m'khamulo anati kwa Iye, Mphunzitsi, uzani mbale wanga agawane ndi ine chuma chamasiye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Munthu wina pakati pa anthu onse aja adapempha Yesu kuti, “Aphunzitsi, takandiwuzirani mbale wanga kuti andigaŵireko chuma chamasiye.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Munthu wina mʼgulu la anthu anati kwa Iye, “Aphunzitsi, muwuzeni mʼbale wanga andigawireko chuma chamasiye.” Onani mutuwo |