Luka 11:53 - Buku Lopatulika53 Ndipo pamene Iye anatuluka m'menemo, alembi ndi Afarisi anayamba kumuumiriza Iye kolimba, ndi kumfunsa zinthu zambiri; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201453 Ndipo pamene Iye anatuluka m'menemo, alembi ndi Afarisi anayamba kumuumiriza Iye kolimba, ndi kumtompha Iye ndi zinthu zambiri; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa53 Pamene Yesu adatuluka m'nyumbamo, aphunzitsi a Malamulo pamodzi ndi Afarisi adayamba kumzonda ndi kumpanikiza ndi mafunso ambiri ozunguza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero53 Pamene Yesu anachokamo, Afarisi ndi aphunzitsi a Malamulo anayamba kumamutsutsa koopsa ndi kumupanikiza ndi mafunso, Onani mutuwo |