Luka 11:27 - Buku Lopatulika27 Ndipo kunali, pakunena izi Iye, mkazi wina mwa khamu la anthu anakweza mau, nati kwa Iye, Yodala mimba imene idakubalani, ndi mawere amene munayamwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201427 Ndipo kunali, pakunena izi Iye, mkazi wina mwa khamu la anthu anakweza mau, nati kwa Iye, Yodala mimba imene idakubalani, ndi mawere amene munayamwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa27 Pamene Yesu ankalankhula zimenezi, mai wina pakati pa anthu ambiri aja adakweza mau namuuza kuti, “Ngwodala mai amene adabalani nkukuyamwitsani.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero27 Pamene Yesu ankanena zonsezi, mayi wina mʼgulu la anthuwo anafuwula nati, “Ndi wodala amayi amene anakubalani ndi kukulerani!” Onani mutuwo |