Luka 11:23 - Buku Lopatulika23 Iye wosavomerezana ndi Ine atsutsana ndi Ine; ndipo iye wosasonkhanitsa pamodzi ndi Ine amwaza. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201423 Iye wosavomerezana ndi Ine atsutsana ndi Ine; ndipo iye wosasonkhanitsa pamodzi ndi Ine amwaza. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa23 “Munthu wosavomerezana ndi Ine, ndiye kuti ngwotsutsana nane. Ndipo wosandithandiza kusonkhanitsa, ndiye kuti ameneyo ngwomwaza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero23 “Munthu amene sali mbali yanga ndi wotsutsana nane. Ndipo wosandithandiza kusonkhanitsa, ameneyo ndi womwaza. Onani mutuwo |