Luka 11:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo ndani wa inu ali atate, mwana wake akadzampempha mkate, adzampatsa mwala? Kapena nsomba, nadzamninkha njoka m'malo mwa nsomba? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo ndani wa inu ali atate, mwana wake akadzampempha mkate, adzampatsa mwala? Kapena nsomba, nadzamninkha njoka m'malo mwa nsomba? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Ndani mwa atatenu, mwana wake atampempha nsomba, iye nkumupatsa njoka? Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 “Ndani mwa inu abambo, kodi mwana wanu atapempha nsomba, mʼmalo mwake mungamupatse njoka? Onani mutuwo |