Luka 10:36 - Buku Lopatulika36 Uti wa awa atatu, uyesa iwe, anakhala mnansi wa iye uja adagwa m'manja a achifwamba? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201436 Uti wa awa atatu, uyesa iwe, anakhala mnansi wa iye uja adagwa m'manja a achifwamba? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa36 Tsono Yesu adafunsa katswiri wa Malamulo uja kuti, “Inu pamenepa mukuganiza bwanji? Mwa anthu atatuŵa, ndani adakhala ngati mnzake wa munthu uja achifwamba adaamugwirayu?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero36 “Kodi ukuganiza ndi ndani mwa atatuwa, amene anali mnansi wa munthu amene anavulazidwa ndi achifwambawo?” Onani mutuwo |