Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Luka 10:14 - Buku Lopatulika

14 Koma ku Tiro ndi Sidoni kudzapiririka m'chiweruziro, koposa inu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Koma ku Tiro ndi Sidoni kudzapiririka m'chiweruziro, koposa inu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 Koma pa tsiku lachiweruzo, Mulungu adzachitako chifundo polanga Tiro ndi Sidoni, koposa polanga inu.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 Koma adzachita chifundo polanga Turo ndi Sidoni kusiyana ndi inu.

Onani mutuwo Koperani




Luka 10:14
10 Mawu Ofanana  

Ndiponso ndili ndi chiyani ndi inu, Tiro ndi Sidoni, ndi malire onse a Filistiya? Mudzandibwezera chilango kodi? Mukandibwezera chilango msanga, mofulumira, ndidzabwezera chilango chanu pamutu panu.


Atero Yehova, Chifukwa cha zolakwa zitatu za Tiro, kapena zinai, sindidzabweza kulanga kwake; popeza anapereka anthu onse kwa Edomu, osakumbukira pangano lachibale;


Inu nokha ndinakudziwani mwa mabanja onse a padziko lapansi, m'mwemo ndidzakulangani chifukwa cha mphulupulu zanu zonse.


Indetu ndinena kwa inu, kuti, tsiku la kuweruza, mlandu wao wa Sodomu ndi Gomora udzachepa ndi wake wa mudzi umenewo.


Tsoka kwa iwe, Korazini! Tsoka kwa iwe, Betsaida! Chifukwa ngati zamphamvu zimene zachitidwa mwa inu zikadachitidwa mu Tiro ndi mu Sidoni, akadatembenuka mtima kalekale m'ziguduli ndi m'phulusa.


Koma chiweruziro ndi ichi, kuti kuunika kunadza kudziko lapansi, ndipo anthu anakonda mdima koposa kuunika; pakuti ntchito zao zinali zoipa.


Chifukwa chake uli wopanda mau owiringula, munthu iwe, amene uli yense wakuweruza; pakuti m'mene uweruza wina, momwemo udzitsutsa iwe wekha, pakuti iwe wakuweruza, umachita zomwezo.


Ndipo kusadulidwa, kumene kuli kwa chibadwidwe, ngati kukwanira chilamulo, kodi sikudzatsutsa iwe, amene uli nao malembo ndi mdulidwe womwe, ndiwe wolakwira lamulo?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa