Luka 10:12 - Buku Lopatulika12 Ndinena ndi inu kuti tsiku lijalo ku Sodomu kudzapiririka kuposa mudzi umenewo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndinena ndi inu kuti tsiku lijalo ku Sodomu kudzapiririka kuposa mudzi umenewo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Kunena zoona, pa tsiku lachiweruzo, Mulungu adzachitako chifundo polanga Sodomu koposa polanga mudzi umenewo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ine ndikuwuzani kuti adzachita chifundo polanga Sodomu pa tsikulo kusiyana ndi mudziwo. Onani mutuwo |