Luka 1:34 - Buku Lopatulika34 Koma Maria anati kwa mngelo, Ichi chidzachitika bwanji, popeza ine sindidziwa mwamuna? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201434 Koma Maria anati kwa mngelo, Ichi chidzachitika bwanji, popeza ine sindidziwa mwamuna? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa34 Koma Maria adafunsa mngeloyo kuti, “Zimenezi zidzachitika bwanji, popeza kuti sindidziŵa mwamuna?” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero34 Mariya anafunsa mngeloyo kuti, “Izi zingatheke bwanji popeza ine sindidziwa mwamuna?” Onani mutuwo |