Luka 1:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo anthu analikulindira Zekariya, nazizwa ndi kuchedwa kwake mu Kachisimo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo anthu analikulindira Zekariya, nazizwa ndi kuchedwa kwake m'Kachisimo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Nthaŵi yonseyo anthu aja ankadikira Zakariya, nkumadabwa kuti akuchedwa m'Nyumba ya Mulungumo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pa nthawiyi, anthu ankadikira Zakariya ndipo anadabwa chifukwa anatenga nthawi yayitali ali mʼNyumba ya Mulungu. Onani mutuwo |