Levitiko 8:4 - Buku Lopatulika4 Ndipo Mose anachita monga Yehova anamuuza; ndi khamulo linasonkhana pa khomo la chihema chokomanako. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Ndipo Mose anachita monga Yehova anamuuza; ndi khamulo linasonkhana pa khomo la chihema chokomanako. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Mose adachitadi zomwe Chauta adamlamula. Choncho mpingo wonse udasonkhana pa khomo la chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Mose anachita zomwe Yehova anamulamula ndipo gulu la anthu linasonkhana pa khomo la tenti ya msonkhano. Onani mutuwo |