Levitiko 7:8 - Buku Lopatulika8 Ndipo chikopa cha nsembe yopsereza chikhale chakechake cha wansembe, amene anabwera nayo nsembe yopsereza ya munthu aliyense. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Ndipo chikopa cha nsembe yopsereza chikhale chakechake cha wansembe, amene anabwera nayo nsembe yopsereza ya munthu aliyense. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Ndipo wansembe wopereka nsembe yopsereza ya munthu wina aliyense, atenge chikopa cha nsembe yopserezayo kuti chikhale chake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Wansembe wopereka nsembe yopsereza ya munthu wina aliyense, atenge chikopa cha nsembe yopserezayo kuti chikhale chake. Onani mutuwo |