Levitiko 4:5 - Buku Lopatulika5 Ndipo wansembe wodzozedwayo atengeko mwazi wa ng'ombeyo, nabwere nao ku chihema chokomanako; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Ndipo wansembe wodzozedwayo atengeko mwazi wa ng'ombeyo, nabwere nao ku chihema chokomanako; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Kenaka wansembe wodzozedwayo atengeko magazi a ng'ombeyo ndi kubwera nawo ku chihema chamsonkhano. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Kenaka wansembe wodzozedwa atengeko magazi a ngʼombeyo ndi kulowa nawo mu tenti ya msonkhano. Onani mutuwo |