Levitiko 3:4 - Buku Lopatulika4 ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pomwepo okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 ndi impso ziwiri, ndi mafuta ali pomwepo okhala m'chuuno, ndi chokuta cha mphafa chofikira kuimpso. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Apatulenso imso ziŵiri, pamodzi ndi mafuta ake omwe, ndiponso mphumphu ya mafuta akuchiŵindi, ochotsa pamodzi ndi imso zija. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Apatulenso impsyo zonse ziwiri pamodzi ndi mafuta ake omwe ndiponso mafuta okuta chiwindi amene achotsedwa pamodzi ndi impsyo zija. Onani mutuwo |