Levitiko 27:4 - Buku Lopatulika4 Koma akakhala wamkazi, umuyesere wa masekeli makumi atatu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma akakhala wamkazi, umuyesere wa masekeli makumi atatu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Munthu wake akakhala wamkazi, mtengo wake ukhale wokwana masekeli asiliva makumi atatu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Ndipo ngati ndi wamkazi, mtengo wake ukhale masekeli makumi atatu. Onani mutuwo |