Levitiko 27:5 - Buku Lopatulika5 Akakhala munthu wa zaka zisanu kufikira wina wa zaka makumi awiri uwayesere, wamwamuna wa masekeli makumi awiri, ndi wamkazi wa masekeli khumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Akakhala munthu wa zaka zisanu kufikira wina wa zaka makumi awiri uwayesere, wamwamuna wa masekeli makumi awiri, ndi wamkazi wa masekeli khumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Akakhala munthu wa zaka zisanu mpaka zaka makumi aŵiri, mtengo wake ukhale wokwana masekeli asiliva makumi aŵiri pa munthu wamwamuna, ndipo khumi pa munthu wamkazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mtengo wa munthu wamwamuna wa zaka zapakati pa zisanu ndi makumi awiri ukhale masekeli makumi awiri ndipo munthu wamkazi ukhale masekeli khumi. Onani mutuwo |