Levitiko 11:3 - Buku Lopatulika3 Nyama iliyonse yogawanika chiboda, nikhala yogawanikadi chiboda, ndi yobzikula, imeneyo muyenera kudya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20143 Nyama iliyonse yogawanika chiboda, nikhala yogawanikadi chiboda, ndi yobzikula, imeneyo muyenera kudya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa3 ‘Nyama zonse zokhala ndi ziboda zogaŵikana, ndi zobzikula, angathe kudya zimenezo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero3 Nyama iliyonse imene ili ndi chipondero chogawikana pakati ndi yobzikula mukhoza kudya. Onani mutuwo |