Levitiko 11:4 - Buku Lopatulika4 Koma izi zokha simuyenera kuzidya mwa zobzikulazo, kapena zogawanika chiboda; ngamira, ingakhale ibzikula, koma yosagawanika chiboda, muziiyesa yodetsedwa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma izi zokha simuyenera kuzidya mwa zobzikulazo, kapena zogawanika chiboda; ngamira, angakhale abzikula, koma yosagawanika chiboda, muziiyesa yodetsedwa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma pakuti pa nyama zobzikula kapena za ziboda zogaŵikanazo, asadye izi: ngamira: imeneyi njonyansa kwa inu pa zachipembedzo, chifukwa ngakhale imabzikula, ziboda zake nzosagaŵikana. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “ ‘Koma pali nyama zina zimene zimabzikula kokha kapena ndi zogawikana zipondero zimene simukuyenera kudya. Nyama zimenezi ndi ngamira, ngakhale imabzikula ilibe zipondero zogawikana. Choncho ndi yodetsedwa, musadye. Onani mutuwo |