Levitiko 1:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo aikadzule ziwalo zake, pamodzi ndi mutu wake ndi mafuta ake; ndi wansembeyo akonze izi pa nkhuni zili pa moto wa paguwa la nsembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo aikadzule ziwalo zake, pamodzi ndi mutu wake ndi mafuta ake; ndi wansembeyo akonze izi pa nkhuni zili pa moto wa pa guwa la nsembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Pambuyo pake ataidula nthulinthuli nyamayo, atengenso mutu ndi mafuta omwe, ndipo aike zonsezo pa nkhuni zimene zili pa guwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kenaka ayidule nyamayo nthulinthuli, ndipo wansembe ayike nthulizo pa guwa, atengenso mutu ndi mafuta omwe, ndipo ayike zonsezi pa nkhuni zimene zikuyaka pa guwa. Onani mutuwo |