Hoseya 9:2 - Buku Lopatulika2 Dwale ndi choponderamo mphesa sizidzawadyetsa, vinyo watsopano adzamsowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Dwale ndi choponderamo mphesa sizidzawadyetsa, vinyo watsopano adzamsowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tirigu ndi mphesa simudzakhala nazo zokwanira. Mudzasoŵanso vinyo woti muzimwa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Malo opunthira tirigu ndi malo opsinyira mphesa sadzadyetsa anthu; adzasowa vinyo watsopano. Onani mutuwo |