Hoseya 7:9 - Buku Lopatulika9 Alendo anatha mphamvu yake osachidziwa iye; imvi zomwe zampakiza osachidziwa iye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Alendo anatha mphamvu yake osachidziwa iye; imvi zomwe zampakiza osachidziwa iye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Alendowo akuŵatha mphamvu, iwo osadziŵako. Akuyamba kumera imvi, iwo osadziŵako. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Alendo atha mphamvu zake, koma iye sakuzindikira. Tsitsi lake layamba imvi koma iye sakudziwa. Onani mutuwo |