Hoseya 7:6 - Buku Lopatulika6 Pakuti asendera nao mtima wao wakunga ng'anjo ya mkate, pokhala alikulalira; wootcha mkate wao agona usiku wonse, m'mawa iyaka ngati moto wa malawi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Pakuti asendera nao mtima wao wakunga ng'anjo ya mkate, pokhala alikulalira; woocha mkate wao agona usiku wonse, m'mawa iyaka ngati moto wa malawi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Mitima yao imatentha ngati uvuni ndi upo wao. Usiku wonse, ukali wao umanyeka, ndipo m'maŵa umayaka ngati moto. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Mitima yawo ili ngati uvuni; amayandikira Mulungu mwachiwembu. Ukali wawo umanyeka usiku wonse, mmawa umayaka ngati malawi a moto. Onani mutuwo |