Hoseya 7:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo Efuremu ali ngati nkhunda yopusa yopanda nzeru; aitanira kwa Ejipito, amuka kwa Asiriya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo Efuremu ali ngati nkhunda yopusa yopanda nzeru; aitanira kwa Ejipito, amuka kwa Asiriya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 “Aefuremu ali ngati nkhunda yopusa, yopanda nzeru. Amaitana Aejipito, namapita ku Asiriya kukapempha chithandizo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 “Efereimu ali ngati nkhunda yopusa yopanda nzeru. Amayitana Igupto namapita ku Asiriya. Onani mutuwo |