Hoseya 4:4 - Buku Lopatulika4 Koma munthu asatsutsane ndi mnzake, kapena kudzudzula mnzake; popeza anthu ako ndiwo akunga otsutsana ndi wansembe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma munthu asatsutsane ndi mnzake, kapena kudzudzula mnzake; popeza anthu ako ndiwo akunga otsutsana ndi wansembe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Chauta akuti, “Wina aliyense asatsutsepo kanthu, wina aliyense asaimbe mnzake mlandu, pakuti mlandu uli pakati pa Ine ndi inu ansembe onyenganu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Koma wina asapeze mnzake chifukwa, wina aliyense asayimbe mlandu mnzake, pakuti anthu ako ali ngati anthu amene amayimba mlandu wansembe. Onani mutuwo |