Hoseya 2:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo ndidzapasula mipesa yake ndi mikuyu yake, imene adanena, Iyi ndi mphotho yanga anandipatsa ondikondawo; ndipo ndidzaisandutsa thengo, ndi nyama zakuthengo zidzaidya. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo ndidzapasula mipesa yake ndi mikuyu yake, imene adanena, Iyi ndi mphotho yanga anandipatsa ondikondawo; ndipo ndidzaisandutsa thengo, ndi nyama za kuthengo zidzaidya. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Ndidzaononga mitengo yake yamphesa ndi yankhuyu imene ankanena kuti, ‘Ameneŵa ndiwo malipiro anga amene zibwenzi zanga zidandipatsa.’ Ndidzaisandutsa malunje, ndipo zilombo zizidzadya kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Ndidzawononga mitengo yake ya mpesa ndi mitengo yake yamkuyu, imene iye ankanena kuti inali malipiro ake ochokera kwa zibwenzi zake. Ndidzayisandutsa chithukuluzi, ndipo zirombo zakuthengo zidzadya zipatsozo. Onani mutuwo |