Hoseya 13:1 - Buku Lopatulika1 Pamene Efuremu analankhula panali kunjenjemera; anadzikweza mu Israele; koma pamene anapalamula mwa Baala, anafa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20141 Pamene Efuremu analankhula panali kunjenjemera; anadzikweza m'Israele; koma pamene anapalamula mwa Baala, anafa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa1 Kale Aefuremu ankati akalankhula, anthu ankachita mantha chifukwa ankalemekezeka m'dziko la Israele, koma adalakwa popembedza Baala, motero adzafa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero1 Kale Efereimu ankati akayankhula, anthu ankanjenjemera; anali wolemekezeka mu Israeli. Koma analakwa popembedza Baala, motero anafa. Onani mutuwo |