Hoseya 12:4 - Buku Lopatulika4 inde, analimbana ndi wamthenga nampambana; analira, nampembedza Iye; anampeza Iye ku Betele, ndi kumeneko Iye analankhula ndi ife; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 inde, analimbana ndi wamthenga nampambana; analira, nampembedza Iye; anampeza Iye ku Betele, ndi kumeneko Iye analankhula ndi ife; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Yakobeyo adalimbana ndi mngelo ndipo adapambana. Adalira napempha madalitso. Mulungu adakumana naye ku Betele, ndipo kumeneko podzera mwa iyeyo adalankhula nafe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 Yakobo analimbana ndi mngelo ndipo anapambana; analira napempha kuti amukomere mtima. Mulungu anakumana naye ku Beteli ndipo anayankhula naye kumeneko, Onani mutuwo |