Hoseya 10:9 - Buku Lopatulika9 Israele, wachimwa kuyambira masiku a Gibea; pomwepo anaimabe; nkhondo ya pa ana a chosalungama siinawapeze ku Gibea. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Israele, wachimwa kuyambira masiku a Gibea; pomwepo anaimabe; nkhondo ya ana a chosalungama siinawapeza ku Gibea. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Chauta akuti, “Kuyambira uchimo wa ku Gibea, Aisraele akhala akuchimwabe. Motero adzagonjetsedwa pa nkhondo ku Gibea komweko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 “Iwe Israeli, wachimwa kuyambira mʼmasiku a Gibeya, ndipo wakhala uli pomwepo. Kodi nkhondo sinagonjetse anthu ochita zoyipa ku Gibeya? Onani mutuwo |