Genesis 9:4 - Buku Lopatulika4 Koma nyama, m'mene muli moyo wake, ndiwo mwazi wake, musadye. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20144 Koma nyama, m'mene muli moyo wake, ndiwo mwazi wake, musadye. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa4 Koma pali chinthu chimodzi chokha chimene simuyenera kudya, ndicho nyama imene ikali ndi magazi. Ndaletsa poti magaziwo ndiwo moyo wake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero4 “Koma musamadye nyama imene ikanali ndi magazi oyenda. Onani mutuwo |