Genesis 9:18 - Buku Lopatulika18 Ndi ana aamuna a Nowa amene anatuluka m'chingalawa ndiwo Semu, ndi Hamu, ndi Yafeti. Hamu ndiye atate wake wa Kanani. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201418 Ndi ana amuna a Nowa amene anatuluka m'chingalawa ndiwo Semu, ndi Hamu, ndi Yafeti: Hamu ndiye atate wake wa Kanani. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa18 Ana a Nowa omwe adatuluka m'chombo muja anali Semu, Hamu ndi Yafeti. Hamu ndiye anali bambo wa Kanani. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero18 Ana aamuna a Nowa amene anatuluka mʼchombo muja anali Semu, Hamu ndi Yafeti. Hamu anali abambo ake a Kanaani. Onani mutuwo |