Genesis 9:17 - Buku Lopatulika17 Ndipo Mulungu anati kwa Nowa, Ichi ndi chizindikiro cha pangano ndalikhazikitsa popangana ndi Ine ndi zamoyo zonse za padziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Ndipo Mulungu anati kwa Nowa, Ichi ndichi chizindikiro cha pangano ndalikhazikitsa popangana ndi Ine ndi zamoyo zonse za pa dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Chimenechi ndi chizindikiro cha chipangano chimene ndachita ndi zamoyo zonse za pa dziko lapansi.” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Choncho Mulungu anati kwa Nowa, “Ichi ndiye chizindikiro cha pangano limene ndalichita pakati pa Ine ndi zamoyo zonse pa dziko lapansi.” Onani mutuwo |