Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 9:10 - Buku Lopatulika

10 ndi zamoyo zonse zili pamodzi ndi inu, zouluka, ng'ombe, ndi zinyama zonse za dziko lapansi, pamodzi ndi inu; zonse zotuluka m'chingalawa, zinyama zonse za dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 ndi zamoyo zonse zili pamodzi ndi inu, zouluka, ng'ombe, ndi zinyama zonse za dziko lapansi, pamodzi ndi inu; zonse zotuluka m'chingalawa, zinyama zonse za dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 ndi zamoyo zonse, mbalame, zoŵeta, nyama zakuthengo, ndi zina zonse zimene zidatuluka nanu m'chombo.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 pamodzi ndi zamoyo zonse, mbalame, ziweto ndi nyama zonse za kuthengo, ndi zonse zimene zinatuluka mʼchombo pamodzi ndi iwe.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 9:10
11 Mawu Ofanana  

Ndipo Mulungu anakumbukira Nowa ndi zamoyo zonse, ndi nyama zonse zimene zinali pamodzi naye m'chingalawamo; ndipo Mulungu anapititsa mphepo padziko lapansi, naphwa madzi;


zinyama zonse, zokwawa zonse, zouluka zonse, ndi zonse zokwawa padziko lapansi, monga mwa mitundu yao, zinatuluka m'chingalawamo.


Ndipo ndidzakhazikitsa pangano langa pamodzi ndi inu; zamoyo zonse sizidzamalizidwanso konse ndi madzi a chigumula; ndipo sikudzakhalanso konse chigumula cha kuononga dziko lapansi.


Ndipo Ine, taonani, Ine ndikhazikitsa pangano langa pamodzi ndi inu, ndi mbeu zanu pambuyo panu;


Yehova achitira chokoma onse; ndi nsoni zokoma zake zigwera ntchito zake zonse.


Ndidzakutomeranso ukhale wanga mokhulupirika, ndipo udzadziwa Yehova.


ndipo sindiyenera Ine kodi kuchitira chifundo Ninive mzinda waukulu uwu; m'mene muli anthu oposa zikwi zana limodzi mphambu zikwi makumi awiri osadziwa kusiyanitsa pakati padzanja lao lamanja ndi lamanzere, ndi zoweta zambiri zomwe?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa