Genesis 8:19 - Buku Lopatulika19 zinyama zonse, zokwawa zonse, zouluka zonse, ndi zonse zokwawa padziko lapansi, monga mwa mitundu yao, zinatuluka m'chingalawamo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 zinyama zonse, zokwawa zonse, zouluka zonse, ndi zonse zokwawa pa dziko lapansi, monga mwa mitundu yao, zinatuluka m'chingalawamo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 Nyama zonse, zokwaŵa zonse, mbalame zonse, ndi zina zonse zoyenda pansi pano zidatuluka m'chombomo m'magulumagulu potsata mitundu yake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Nyama zonse, zokwawa zonse, mbalame zonse, chilichonse choyenda pa dziko lapansi, zinatuluka mʼchombo motsogozana monga mwa mitundu yawo. Onani mutuwo |