Genesis 8:14 - Buku Lopatulika14 Mwezi wachiwiri tsiku la makumi awiri kudza asanu ndi awiri la mwezi, lidauma dziko lapansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Mwezi wachiwiri tsiku la makumi awiri kudza asanu ndi awiri la mwezi, lidauma dziko lapansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Pa tsiku la 27 mwezi wachiŵiri, dziko lonse lapansi linali litauma kotheratu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Pokwana tsiku la 27 la mwezi wachiwiri dziko lapansi linawumiratu. Onani mutuwo |
Ndipo kunali chaka cha makumi atatu mphambu zisanu ndi ziwiri cha kumtenga ndende Yehoyakini mfumu ya Yuda, mwezi wakhumi ndi ziwiri, tsiku la makumi awiri mphambu asanu ndi awiri la mwezi, Evili-Merodaki mfumu ya Babiloni anamuweramutsa mutu wake wa Yehoyakini mfumu ya Yuda atuluke m'kaidi, chaka cholowa iye ufumu wake;