Genesis 8:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo analinda masiku ena asanu ndi awiri; natulutsanso njiwayo m'chingalawamo; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo analinda masiku ena asanu ndi awiri; natulutsanso njiwayo m'chingalawamo; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Atadikira masiku asanu ndi aŵiri ena, adaitulutsanso nkhunda ija m'chombo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Choncho anadikirabe masiku ena asanu ndi awiri ndipo anatulutsanso nkhundayo mʼchombo muja. Onani mutuwo |