Genesis 7:9 - Buku Lopatulika9 zinalowa ziwiriziwiri kwa Nowa m'chingalawamo, yamphongo ndi yaikazi, monga momwe Mulungu anamlamulira Nowa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 zinalowa ziwiriziwiri kwa Nowa m'chingalawamo, yamphongo ndi yaikazi, monga momwe Mulungu anamlamulira Nowa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Nowa adaloŵa nazo m'chombo, monga Mulungu adaalamulira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ndipo Nowa anatenga ziwiriziwiri, yayimuna ndi yayikazi monga anamulamulira Mulungu. Onani mutuwo |