Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 7:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo panali pamene anapita masiku asanu ndi awiri, madzi a chigumula anali padziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo panali pamene anapita masiku asanu ndi awiri, madzi a chigumula anali pa dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Patangopita masiku asanu ndi aŵiri, chigumula chidafika pa dziko lonse lapansi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Patapita masiku asanu ndi awiri chigumula chinabwera pa dziko lapansi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 7:10
7 Mawu Ofanana  

Ndine, taonani, ndipo Ine ndidzadzetsa chigumula cha madzi padziko lapansi, kuti chiononge zamoyo zonse, m'mene muli mpweya wa moyo pansi pathambo; zinthu zonse za m'dziko lapansi zidzafa.


Pakuti akapita masiku asanu ndi awiri Ine ndidzavumbitsa mvula padziko lapansi masiku makumi anai usana ndi usiku; ndi zinthu zamoyo zonse zomwe ndazipanga ndidzaziononga padziko lapansi.


zinalowa ziwiriziwiri kwa Nowa m'chingalawamo, yamphongo ndi yaikazi, monga momwe Mulungu anamlamulira Nowa.


Amene anakwatulidwa isanafike nyengo yao, chigumula chinakokolola kuzika kwao;


Anadya, anamwa, anakwatira, anakwatiwa, kufikira tsiku lija Nowa analowa m'chingalawa, ndipo chinadza chigumula, nkuwaononga onsewo.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa