Genesis 7:22 - Buku Lopatulika22 zonse zimene m'mphuno zao munali mpweya wa mzimu wa moyo, zonse zinali pamtunda, zinafa. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 zonse zimene m'mphuno zao munali mpweya wa mzimu wa moyo, zonse zinali pamtunda, zinafa. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Zamoyo zonse za pa dziko lapansi zidafa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Chilichonse chamoyo, chokhala pa mtunda chinafa. Onani mutuwo |