Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 6:21 - Buku Lopatulika

21 Ndipo iwe udzitengereko wekha zakudya zonse zodyedwa, nudzisonkhanitsire izi wekha: ndipo zidzakhala zakudya za iwe ndi za iwo.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

21 Ndipo iwe udzitengereko wekha zakudya zonse zodyedwa, nudzisonkhanitsire izi wekha: ndipo zidzakhala zakudya za iwe ndi za iwo.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

21 Udzatengenso zakudya za mtundu uliwonse kuti inu ndi nyamazo muzidzadya.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

21 Udzatengenso chakudya cha mtundu uliwonse ndi kuchisunga kuti inu ndi nyamazo muzidzadya.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 6:21
9 Mawu Ofanana  

Amkonzeratu khwangwala chakudya chake ndani, pamenepo ana ake afuulira kwa Mulungu, naulukauluka osowa chakudya?


Pakuti mapiri aiphukitsira chakudya, kumene zisewera nyama zonse zakuthengo.


Ndiye wakupatsa nyama zonse chakudya; pakuti chifundo chake nchosatha.


Muolowetsa dzanja lanu, nimukwaniritsira zamoyo zonse chokhumba chao.


Amene apatsa zoweta chakudya chao, ana a khwangwala alikulira.


Njira yao ikhale ya mdima ndi yoterera, ndipo mngelo wa Yehova awalondole.


Yang'anirani mbalame za kumwamba, kuti sizimafesa ai, kapena sizimatema ai, kapena sizimatutira m'nkhokwe; ndipo Atate wanu wa Kumwamba azidyetsa. Nanga inu mulibe kusiyana nazo kuziposa kodi?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa