Genesis 6:10 - Buku Lopatulika10 Ndipo Nowa anabala ana aamuna atatu: Semu, Hamu ndi Yafeti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201410 Ndipo Nowa anabala ana amuna atatu, Semu, Hamu ndi Yafeti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa10 Anali ndi ana aamuna atatu: Semu, Hamu ndi Yafeti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero10 Nowa anabereka ana aamuna atatu: Semu, Hamu ndi Yafeti. Onani mutuwo |