Genesis 50:7 - Buku Lopatulika7 Ndipo Yosefe anapita kukaika atate wake; ndipo anakwera pamodzi ndi akapolo onse a Farao, ndi akulu a pa mbumba yake, ndi akulu onse a m'dziko la Ejipito, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Ndipo Yosefe anapita kukaika atate wake; ndipo anakwera pamodzi ndi akapolo onse a Farao, ndi akulu a pa mbumba yake, ndi akulu onse a m'dziko la Ejipito, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Yosefe adapita kukaika bambo wake. Ndipo nduna zonse za Farao, akuluakulu a bwalo, ndi anthu ena otchuka a ku Ejipito adamperekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Kotero Yosefe anapita kukayika abambo ake. Nduna zonse za Farao, akuluakulu a bwalo lake ndi akuluakulu a ku Igupto, anapita naye pamodzi. Onani mutuwo |