Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 50:4 - Buku Lopatulika

4 Atapita masiku akumlira iye, Yosefe anati kwa mbumba ya Farao, kuti, Ngatitu ndapeza ufulu pamaso panu, nenanitu m'makutu a Farao kuti,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

4 Atapita masiku akumlira iye, Yosefe anati kwa mbumba ya Farao, kuti, Ngatitu ndapeza ufulu pamaso panu, nenanitu m'makutu a Farao kuti,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

4 Yosefe atatha kulira maliro a bambo wake, adauza nduna za Farao kuti, “Chonde mundikomere mtima, Farao mukamuuze kuti,

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

4 Yosefe atatha kulira maliro a abambo ake, anayankhula kwa nduna za Farao nati, “Ngati mungandikomere mtima, chonde mundiyankhulire kwa Farao kumuwuza kuti,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 50:4
4 Mawu Ofanana  

Mbuyanga, ngatitu ndi ndikapeza ufulu pamaso panu, musapitiriretu pa kapolo wanu;


Ndipo anatha masiku ake makumi anai a iye; chifukwa chomwecho amatsiriza masiku akukonza thupi; ndipo Aejipito anamlira iye masiku makumi asanu ndi awiri.


Atate wanga anandilumbiritsa ine, kuti, Taona, ndilinkufa; m'manda m'mene ndadzikonzeratu ndekha m'dziko la Kanani, m'menemo udzandiika ine. Tsopano mundiloletu, ndikwereko, ndipite, ndikaike atate wanga, nditatero ndidzabweranso.


nafika popenyana ndi chipata cha mfumu; popeza sanathe munthu kulowa kuchipata cha mfumu wovala chiguduli.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa