Genesis 50:22 - Buku Lopatulika22 Ndipo Yosefe anakhala mu Ejipito, iye, ndi mbumba ya atate wake; ndipo Yosefe anakhala ndi moyo zaka zana limodzi ndi khumi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Ndipo Yosefe anakhala m'Ejipito, iye, ndi mbumba ya atate wake; ndipo Yosefe anakhala ndi moyo zaka zana limodzi ndi khumi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Yosefe adakhala ku Ejipito pamodzi ndi mbumba ya atate ake. Pamene ankamwalira nkuti ali wa zaka 110. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Yosefe anakhala mu Igupto pamodzi ndi banja lonse la abambo ake. Anakhala ndi moyo zaka 110 Onani mutuwo |