Genesis 50:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo Yosefe anauza akapolo ake asing'anga kuti akonze atate wake ndi mankhwala osungira thupi: ndipo asing'anga anakonza Israele. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo Yosefe anauza akapolo ake asing'anga kuti akonze atate wake ndi mankhwala osungira thupi: ndipo asing'anga anakonza Israele. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono Yosefeyo adalamula asing'anga kuti akonze ndi mankhwala mtembo wa bambo wake, kuti usaole, ndipo iwowo adachitadi zimenezo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo Yosefe analamula antchito ake a chipatala kuti akonze thupi la Israeli ndi mankhwala kuti lisawole. Kotero antchitowo anakonzadi thupilo. Onani mutuwo |