Genesis 50:16 - Buku Lopatulika16 Ndipo anatumiza mthenga kwa Yosefe kuti, Atate wathu asanafe analamulira, kuti, Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201416 Ndipo anatumiza mthenga kwa Yosefe kuti, Atate wathu asanafe analamulira, kuti, Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa16 Motero adatumiza mau kwa Yosefe kuti, “Atate anu asanafe adanena mau akuti, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero16 Motero anatumiza mawu kwa Yosefe kuti, “Abambo anu anasiya malangizo asanafe nati: Onani mutuwo |