Genesis 5:5 - Buku Lopatulika5 Masiku ake onse anakhala ndi moyo Adamu anali zaka mazana asanu ndi anai, kudza makumi atatu; ndipo anamwalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Masiku ake onse anakhala ndi moyo Adamu anali zaka mazana asanu ndi anai, kudza makumi atatu; ndipo anamwalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Adamwalira ali wa zaka 930. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Zaka zonse za Adamu zinali 930 ndipo anamwalira. Onani mutuwo |