Genesis 5:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo Metusela anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi atatu ndi zisanu ndi ziwiri, nabala Lameki; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo Metusela anakhala ndi moyo zaka zana kudza makumi asanu ndi atatu ndi zisanu ndi ziwiri, nabala Lameki; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Metusela ali wa zaka 187, adabereka mwana dzina lake Lameki, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Pamene Metusela anali ndi zaka 187, anabereka Lameki. Onani mutuwo |