Genesis 5:26 - Buku Lopatulika26 ndipo Metusela anakhala ndi moyo, atabala Lameki, zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi atatu ndi ziwiri, nabala ana aamuna ndi aakazi: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 ndipo Metusela anakhala ndi moyo, atabala Lameki, zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi atatu ndi awiri, nabala ana aamuna ndi aakazi: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 782. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Ndipo atabadwa Lameki, Metusela anakhala ndi moyo zaka zina 782 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwo |