Genesis 5:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo Kenani anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi awiri, ndipo anabala Mahalalele: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo Kenani anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi awiri, ndipo anabala Mahalalele: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Kenani ali wa zaka 70, adabereka mwana dzina lake Mahalalele, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Pamene Kenani anali ndi zaka 70, anabereka Mahalaleli. Onani mutuwo |