Genesis 5:11 - Buku Lopatulika11 Masiku ake onse a Enosi anali mazana asanu ndi anai kudza zisanu; ndipo anamwalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Masiku ake onse a Enosi anali mazana asanu ndi anai kudza zisanu; ndipo anamwalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Adamwalira ali wa zaka 905. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Zaka zonse za Enosi pamodzi zinali 905 ndipo anamwalira. Onani mutuwo |